Chikondi Chenicheni​—Mawu Oyamba

Chikondi Chenicheni​—Mawu Oyamba

Padziko lapansi pali miyambo yosiyanasiyana imene anthu amatsatira akakhala pa chibwenzi, choncho mukamaonera vidiyoyi maganizo anu akhale pa mfundo za m’Baibulo chifukwa n’zothandiza kwa anthu azikhalidwe zonse.