NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) May 2025
NKHANI YOPHUNZIRA 19
Muzitsanzira Angelo Okhulupirika
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 14-20, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 20
Muzidalira Yehova Kuti Azikutonthozani
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 21-27, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 21
Tiziyembekezera Mzinda Umene Sudzawonongeka
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 28–August 3, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 22
Dzina la Yehova Ndi Lofunika Kwambiri kwa Yesu
Idzaphunziridwa mlungu woyambira August 4-10, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 23
Dzina la Yehova Ndi Lofunika Kwambiri kwa Ife
Idzaphunziridwa mlungu woyambira August 11-17, 2025.
Muzikonzekeretsa Mtima Wanu
Kodi tingakonzekeretse bwanji mtima wathu tikamaphunzira Baibulo?