NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) July 2025
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira September 15–October 12, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 28
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupempha Malangizo?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 15-21, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 29
Zimene Tingachite Kuti Tizipereka Malangizo Abwino
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 22-28, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 30
Kodi Mfundo Zoyambirira za M’Baibulo Zingakuthandizenibe Masiku Ano?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 29–October 5, 2025.
NKHANI YOPHUNZIRA 31
Kodi ‘Mwaphunzira Chinsinsi’ Chokhala Wokhutira?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira October 6-12, 2025.
MBIRI YA MOYO WANGA
“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”
Pa zaka 40 zapitazi, M’bale Philip Brumley wakhala ndi mwayi wogwira ntchito ndi abale m’maofesi a nthambi padziko lonse pa nkhani zamalamulo komanso kuonekera m’makhoti osiyanasiyana ndiponso pamaso pa akuluakulu a boma. Iye akuti zimenezi zamuthandiza kutsimikizira kuti Yehova ndi amene amapereka mphamvu komanso luso kwa atumiki ake kuti apambane.
Kodi Mukudziwa?
Kodi ansembe a pakachisi ankatani ndi magazi a nyama zomwe zaperekedwa nsembe paguwa?
MFUNDO ZOTHANDIZA POPHUNZIRA
Muziuza Ena Zimene Mwaphunzira
Kuuza ena zimene taphunzira kungatithandize kuti tizikumbukira komanso kumvetsa bwino zinthu.