Chiwerewere
Khalidwe lopanda manyazi; khalidwe limene limadetsa munthu; chigololo
Eks 20:13-17; Mko 7:21-23; 1Ak 6:9, 10, 18; Aga 5:19, 21; Aef 5:5; 1Pe 4:3
Onaninso Le 20:10; Miy 6:32; Aro 13:13; Aef 4:19; 5:3; 2Pe 2:2, 7, 8, 18, 19
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Ge 39:7-12—Mkazi wa Potifara ankamukakamiza Yosefe mobwerezabwereza kuti agone naye, koma iye nthawi zonse ankakana
2Sa 12:7-14—Mfumu Davide atachita chigololo ndi Bati-seba, banja lake linavutika kwa zaka zambiri