Zokhudza Kusunga Chinsinsi

Pofuna kukuthandizani kuti musamavutike kuchita zinthu pawebusaiti yathu, timagwiritsa ntchito ma cookies ndiponso njira zina zamakono zofanana ndi zimenezi. Ma cookies ena amathandiza kuti webusaiti yathu izigwira bwino ntchito ndipo sizingatheke kuwakana. Mukhoza kuvomereza kapena kukana ma cookies ena owonjezera, omwe cholinga chake ndi kungokuthandizani kuti musamavutike kuchita zinthu zina pawebusaiti. Sitidzagulitsa kapena kugwiritsa ntchito mauthenga amenewa pofuna kutsatsa malonda. Kuti mudziwe zambiri, werengani Ndondomeko ya Padziko Lonse ya Mmene Timagwiritsira Ntchito ma Cookies ndi Njira Zina Zamakono. Mukhoza kusintha ma settings nthawi ina iliyonse popita pa Zokhudza Kusunga Chinsinsi.

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti mavuto amene timakumana nawo si chilango chochokera kwa Mulungu?

Lemba: Yak. 1:13

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani timavutika?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: N’chifukwa chiyani timavutika?

Lemba: 1 Yoh. 5:19

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amamva bwanji akamationa tikuvutika?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi Mulungu amamva bwanji akamationa tikuvutika?

Lemba: Yes. 63:9

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu adzathetsa bwanji mavutowa?