December 11-17
YOBU 25-27
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Sitifunika Kukhala Angwiro Kuti Tikhale Okhulupirika”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 26:14—Kodi zinthu zochepa zokhudza chilengedwe zomwe timadziwa zimatithandiza kumvetsa chiyani zokhudza Yehova? (w16.11 9 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 25:1–26:14 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni mmene angapezere nkhani yomwe yamusangalatsa pa jw.org. (th phunziro 17)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 13 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kukhulupirika Kumagwirizana ndi Zimene Timaganiza”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 3 ¶4-11
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero